Ulendo wa mayi wopita kumadzi... Lowani nawo ulendowu!
Zingakhale zovuta kulingalira mmene moyo ukanakhala popanda madzi aukhondo. Koma simuyenera kuganiza, chifukwa tidzakutengerani paulendo wa amayi kukafuna madzi. Lowani nawo wodzipereka ku FARM STEW, Wyatt Johnston, paulendo wakumasuka ku zolemetsa ndi matenda. Mphatso zanu zapangitsa kuti izi zitheke. Zikomo!!